1 Mbiri 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Onsewa anali asilikali okonzeka kumenya nkhondo. Iwo anapita ndi mtima wonse ku Heburoni kukaveka Davide ufumu wa Isiraeli yense. Aisiraeli ena onse otsala nawonso ankagwirizana nazo ndi mtima wonse zoti Davide avekedwe ufumu.+
38 Onsewa anali asilikali okonzeka kumenya nkhondo. Iwo anapita ndi mtima wonse ku Heburoni kukaveka Davide ufumu wa Isiraeli yense. Aisiraeli ena onse otsala nawonso ankagwirizana nazo ndi mtima wonse zoti Davide avekedwe ufumu.+