38 Onsewa anali amuna ankhondo, okhalira limodzi pamzere wa omenya nkhondo. Iwo anapita ndi mtima wathunthu+ ku Heburoni kukalonga Davide kukhala mfumu ya Isiraeli yense. Ndiponso Aisiraeli ena onse otsala anali ndi mtima umodzi wolonga Davide ufumu.+