Salimo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+