Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 21:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Ichi n’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu n’kuperekedwa kwa mtundu wobala zipatso zake.+

  • Afilipi 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Si kuti mtima wanga uli pa mphatsoyo ayi,+ koma ndikufunitsitsa kuti mulandire madalitso+ amene adzawonjezere phindu pa zimene muli nazo.

  • Chivumbulutso 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mtsinjewo unali kudutsa pakati pa msewu waukulu wa mumzindawo. Kumbali iyi ya mtsinjewo ndi kumbali inayo, kunali mitengo+ ya moyo yobala zipatso zokolola maulendo 12, ndipo inali kubala zipatso mwezi uliwonse.+ Masamba a mitengoyo anali ochiritsira mitundu ya anthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena