Genesis 27:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho, Esau anasunga chidani kwa Yakobo mumtima mwake.+ Anamuda chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa. Iye anapitiriza kunena mumtima mwake+ kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha m’bale wanga Yakobo.”+ Genesis 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndapota nanu, ndipulumutseni+ ku dzanja la m’bale wanga, dzanja la Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, ndithu angavulaze ineyo,+ akaziwa pamodzi ndi anawa.
41 Choncho, Esau anasunga chidani kwa Yakobo mumtima mwake.+ Anamuda chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa. Iye anapitiriza kunena mumtima mwake+ kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha m’bale wanga Yakobo.”+
11 Ndapota nanu, ndipulumutseni+ ku dzanja la m’bale wanga, dzanja la Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, ndithu angavulaze ineyo,+ akaziwa pamodzi ndi anawa.