Genesis 27:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho, Esau anasunga chidani kwa Yakobo mumtima mwake.+ Anamuda chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa. Iye anapitiriza kunena mumtima mwake+ kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha m’bale wanga Yakobo.”+ Salimo 112:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtima wake sungagwedezeke,+ ndipo sadzachita mantha,+ע [ʽAʹyin]Pamapeto pake adzayang’ana adani ake atagonjetsedwa.+ Miyambo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’bale amene walakwiridwa amaposa mzinda wolimba,+ ndipo pali mikangano imene imakhala ngati mtengo wotsekera pachipata cha nsanja yokhalamo.+
41 Choncho, Esau anasunga chidani kwa Yakobo mumtima mwake.+ Anamuda chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa. Iye anapitiriza kunena mumtima mwake+ kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha m’bale wanga Yakobo.”+
8 Mtima wake sungagwedezeke,+ ndipo sadzachita mantha,+ע [ʽAʹyin]Pamapeto pake adzayang’ana adani ake atagonjetsedwa.+
19 M’bale amene walakwiridwa amaposa mzinda wolimba,+ ndipo pali mikangano imene imakhala ngati mtengo wotsekera pachipata cha nsanja yokhalamo.+