Salimo 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinafunsa kwa Yehova ndipo iye anandiyankha,+Pakuthawathawa kwanga konse iye anandilanditsa.+ Salimo 107:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+