Salimo 18:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wachiwawa.+ Salimo 144:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+
48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wachiwawa.+
10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+