2 Samueli 22:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Iye amandichotsa pakati pa adani anga.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wochita zachiwawa.+ Salimo 140:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Inu Yehova, ndilanditseni kwa anthu oipa.+Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa,+
49 Iye amandichotsa pakati pa adani anga.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wochita zachiwawa.+