Salimo 18:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wachiwawa.+ Salimo 71:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni m’manja mwa woipa,+Ndipulumutseni m’manja mwa munthu wochita zinthu mopanda chilungamo komanso mopondereza.+
48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wachiwawa.+
4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni m’manja mwa woipa,+Ndipulumutseni m’manja mwa munthu wochita zinthu mopanda chilungamo komanso mopondereza.+