2 Samueli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anthu onse anayamba kukangana m’mafuko onse a Isiraeli kuti: “Mfumuyi ndi imene inatilanditsa m’manja mwa adani athu,+ ndipo ndi mfumu yomweyi imene inatipulumutsa m’manja mwa Afilisiti. Tsopano yachoka m’dziko lino kuthawa Abisalomu.+
9 Ndiyeno anthu onse anayamba kukangana m’mafuko onse a Isiraeli kuti: “Mfumuyi ndi imene inatilanditsa m’manja mwa adani athu,+ ndipo ndi mfumu yomweyi imene inatipulumutsa m’manja mwa Afilisiti. Tsopano yachoka m’dziko lino kuthawa Abisalomu.+