Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ukatero, tikamuukire kumene tikudziwa kuti tikhoza kum’peza,+ ndipo tikam’fikira ngati mmene mame+ amagwera pansi. Pamenepo sipadzakhala aliyense wopulumuka, iyeyo ngakhale amuna onse amene ali naye.

  • Salimo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+

      Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+

      Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+

  • Salimo 17:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chifukwa cha anthu oipa amene akundipondereza.

      Adani a moyo wanga atsala pang’ono kundipeza.+

  • Salimo 59:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Inu Mulungu wanga, ndilanditseni kwa adani anga.+

      Nditetezeni kwa anthu amene akundiukira.+

  • Salimo 140:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Inu Yehova, ndithandizeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+

      Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa.+

      Nditetezeni kwa anthu amene andikonzera chiwembu kuti andikankhe ndi kundigwetsa.+

  • Mateyu 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena