Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+