Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+ 2 Samueli 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+ 1 Mbiri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala akapolo a Davide.+ Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+
14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
13 Choncho anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala akapolo a Davide.+ Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+