Genesis 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova anamuyankha kuti: “M’mimba mwako+ muli mitundu iwiri ya anthu, ndipo mitundu iwiri imene idzatuluka m’mimba mwakoyo idzakhala yosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamng’ono.”+ Genesis 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+
23 Yehova anamuyankha kuti: “M’mimba mwako+ muli mitundu iwiri ya anthu, ndipo mitundu iwiri imene idzatuluka m’mimba mwakoyo idzakhala yosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamng’ono.”+
40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+