Genesis 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova anamuyankha kuti: “M’mimba mwako+ muli mitundu iwiri ya anthu, ndipo mitundu iwiri imene idzatuluka m’mimba mwakoyo idzakhala yosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamng’ono.”+ 2 Samueli 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
23 Yehova anamuyankha kuti: “M’mimba mwako+ muli mitundu iwiri ya anthu, ndipo mitundu iwiri imene idzatuluka m’mimba mwakoyo idzakhala yosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamng’ono.”+
14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+