1 Mbiri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala akapolo a Davide.+ Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+ Salimo 60:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi thandizo la Mulungu, tidzalandira mphamvu,+Ndipo Mulungu adzapondereza adani athu.+
13 Choncho anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala akapolo a Davide.+ Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+