2 Samueli 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali mʼdera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti ankapereka msonkho kwa iye. Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+
6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali mʼdera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti ankapereka msonkho kwa iye. Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+