Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo mʼmanja mwanu,+ ndipo inu mudzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzalimbane ndi inu+ mpaka mutawawononga.+ 2 Samueli 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali ku Edomu. Mu Edomu monse anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+
24 Adzapereka mafumu awo mʼmanja mwanu,+ ndipo inu mudzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzalimbane ndi inu+ mpaka mutawawononga.+
14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali ku Edomu. Mu Edomu monse anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+