1 Mbiri 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anamanga midzi ya asilikali m’dera la Asiriya a ku Damasiko,+ ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho kwa iye.+ Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
6 Ndiyeno Davide anamanga midzi ya asilikali m’dera la Asiriya a ku Damasiko,+ ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho kwa iye.+ Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+