1 Mbiri 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse+ pamaso pako. Ndidzakupangira dzina+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali padziko lapansi.+
8 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse+ pamaso pako. Ndidzakupangira dzina+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali padziko lapansi.+