Genesis 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndidzatulutsa mtundu waukulu mwa iwe. Ndidzakudalitsa ndi kukuza dzina lako, ndipo iwe ukhale dalitso+ kwa ena. 1 Samueli 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno akalonga+ a Afilisiti akatuluka kudzamenya nkhondo, Davide anali kuchita zinthu mwanzeru kwambiri+ mwa atumiki onse a Sauli, moti dzina la Davide linatchuka kwambiri.+ Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+ Luka 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Watsitsa anthu amphamvu+ zawo pamipando yachifumu, ndipo wakweza anthu wamba.+
2 Ine ndidzatulutsa mtundu waukulu mwa iwe. Ndidzakudalitsa ndi kukuza dzina lako, ndipo iwe ukhale dalitso+ kwa ena.
30 Ndiyeno akalonga+ a Afilisiti akatuluka kudzamenya nkhondo, Davide anali kuchita zinthu mwanzeru kwambiri+ mwa atumiki onse a Sauli, moti dzina la Davide linatchuka kwambiri.+