Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+
8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+