2 Mafumu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero. 2 Mbiri 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Gulu lankhondo la Siriyalo linalowa m’dzikolo ndi amuna ochepa,+ koma Yehova anapereka m’manja mwawo gulu lankhondo lalikulu kwambiri+ popeza iwo anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo. Asiriyawo anaperekanso chiweruzo kwa Yehoasi.+
6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero.
24 Gulu lankhondo la Siriyalo linalowa m’dzikolo ndi amuna ochepa,+ koma Yehova anapereka m’manja mwawo gulu lankhondo lalikulu kwambiri+ popeza iwo anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo. Asiriyawo anaperekanso chiweruzo kwa Yehoasi.+