2 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehu atangoyamba kulimbana ndi a m’nyumba ya Ahabu,+ anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya,+ omwe anali atumiki a Ahaziya, ndipo anawapha.+ Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake. Habakuku 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+
8 Yehu atangoyamba kulimbana ndi a m’nyumba ya Ahabu,+ anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya,+ omwe anali atumiki a Ahaziya, ndipo anawapha.+
5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake.
12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+