2 Mafumu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano dziwani kuti mawu onse a Yehova otsutsa nyumba ya Ahabu+ amene Yehova analankhula, adzakwaniritsidwa.+ Yehova wachita zimene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Eliya.”+ 2 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+
10 Tsopano dziwani kuti mawu onse a Yehova otsutsa nyumba ya Ahabu+ amene Yehova analankhula, adzakwaniritsidwa.+ Yehova wachita zimene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Eliya.”+
11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+