2 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera apo, Yehu anapha anthu onse a mʼbanja la Ahabu amene anatsala ku Yezereeli komanso anthu ake onse olemekezeka, anzake ndiponso ansembe ake+ mpaka onse anatha.+
11 Kuwonjezera apo, Yehu anapha anthu onse a mʼbanja la Ahabu amene anatsala ku Yezereeli komanso anthu ake onse olemekezeka, anzake ndiponso ansembe ake+ mpaka onse anatha.+