2 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+
11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+