6 Choncho mfumu ya Isiraeli inasonkhanitsa aneneri pamodzi.+ Analipo amuna pafupifupi 400, ndipo inawafunsa kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena ndisapite?” Iwo anayankha kuti: “Pitani,+ ndipo Yehova akapereka mzindawo m’manja mwanu mfumu.”