Ezekieli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa aneneri opusa,+ amene akungolosera zamumtima mwawo+ pamene sanaone chilichonse.+
3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa aneneri opusa,+ amene akungolosera zamumtima mwawo+ pamene sanaone chilichonse.+