Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho mfumu ya Isiraeli inasonkhanitsa aneneri+ pamodzi. Analipo amuna 400, ndipo inawafunsa kuti: “Kodi tipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena tisapite?”+ Iwo anayankha kuti: “Pitani, ndipo Mulungu woona akapereka mzindawo m’manja mwanu mfumu.”

  • Yeremiya 5:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+

  • Yeremiya 23:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “Chotero ndikutsutsana ndi aneneriwo+ chifukwa aliyense wa iwo akuba mawu anga kwa mnzake,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena