Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+ Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa. 2 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti onsewo adzaweruzidwe chifukwa sanakhulupirire choonadi,+ koma anakonda zosalungama.+ 2 Timoteyo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti idzafika nthawi imene anthu sadzafunanso chiphunzitso cholondola,+ koma mogwirizana ndi zilakolako zawo, adzadzipezera aphunzitsi kuti amve zowakomera m’khutu.+
10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
3 Pakuti idzafika nthawi imene anthu sadzafunanso chiphunzitso cholondola,+ koma mogwirizana ndi zilakolako zawo, adzadzipezera aphunzitsi kuti amve zowakomera m’khutu.+