Deuteronomo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Koma mneneri amene adzadzikuza mwa kulankhula m’dzina langa mawu amene sindinamulamule kuti alankhule,+ kapena kulankhula m’dzina la milungu ina,+ mneneri ameneyo afe ndithu.+ Yeremiya 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Kunena za aneneriwo amene akulosera m’dzina langa ngakhale kuti sindinawatume, amenenso akunena kuti lupanga kapena njala sizidzafika m’dziko lino, ndidzawawononga ndi lupanga ndiponso njala.+ Ezekieli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+ Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+
20 “‘Koma mneneri amene adzadzikuza mwa kulankhula m’dzina langa mawu amene sindinamulamule kuti alankhule,+ kapena kulankhula m’dzina la milungu ina,+ mneneri ameneyo afe ndithu.+
15 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Kunena za aneneriwo amene akulosera m’dzina langa ngakhale kuti sindinawatume, amenenso akunena kuti lupanga kapena njala sizidzafika m’dziko lino, ndidzawawononga ndi lupanga ndiponso njala.+
2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli.+ Uuze amene akulosera zam’mutu mwawo+ kuti, ‘Mvetserani mawu a Yehova.+
24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+