Ezekieli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli+ ndipo anthu amene akulosera zamʼmutu mwawo+ uwauze kuti, ‘Imvani mawu a Yehova.
2 “Iwe mwana wa munthu, losera zokhudza aneneri a mu Isiraeli+ ndipo anthu amene akulosera zamʼmutu mwawo+ uwauze kuti, ‘Imvani mawu a Yehova.