Yeremiya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera zinthu zabodza mʼdzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo ndi masomphenya abodza, maulosi opanda pake ndi chinyengo chamumtima mwawo.+ Yeremiya 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa inu.+ Iwo akungokupusitsani.* Iwo akulankhula masomphenya amumtima mwawo,+Osati ochokera mʼkamwa mwa Yehova.+
14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera zinthu zabodza mʼdzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo ndi masomphenya abodza, maulosi opanda pake ndi chinyengo chamumtima mwawo.+
16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa inu.+ Iwo akungokupusitsani.* Iwo akulankhula masomphenya amumtima mwawo,+Osati ochokera mʼkamwa mwa Yehova.+