Yeremiya 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 chifukwa cha zoipa zonse zimene ana a Isiraeli+ ndi ana a Yuda+ achita ndi kundikhumudwitsa nazo.+ Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo,+ aneneri awo,+ amuna a mu Yuda ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu. Mateyu 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe.
32 chifukwa cha zoipa zonse zimene ana a Isiraeli+ ndi ana a Yuda+ achita ndi kundikhumudwitsa nazo.+ Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo,+ aneneri awo,+ amuna a mu Yuda ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu.
20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe.