Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Masiku ake onse, sanasiye machimo onse a Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+

  • 2 Mafumu 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamalo okwezeka onsewo, iwo anapitiriza kufukizapo nsembe yautsi, mofanana ndi mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa m’dzikolo chifukwa cha Aisiraeliwo. Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa zokwiyitsa+ Yehova.

  • 2 Mafumu 17:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+

  • Yeremiya 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+

  • Yeremiya 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Yehova wa makamu, Wokubzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a m’nyumba ya Isiraeli+ ndi a m’nyumba ya Yuda achita ndi kundikhumudwitsa nazo pofukizira Baala nsembe zautsi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena