2 Mafumu 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Masiku ake onse, sanasiye kuchita machimo onse amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+
18 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Masiku ake onse, sanasiye kuchita machimo onse amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+