1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ 1 Mafumu 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pambuyo pa zimenezi, Yerobowamu sanasiyebe njira yake yoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kukhala ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye anali kum’patsa mphamvu+ mwa kunena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
33 Pambuyo pa zimenezi, Yerobowamu sanasiyebe njira yake yoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kukhala ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye anali kum’patsa mphamvu+ mwa kunena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”