Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+

  • Salimo 78:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+

      Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+

  • Yeremiya 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+

  • Yeremiya 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chiyani wanenera m’dzina la Yehova kuti, ‘Nyumba iyi idzafanana ndi nyumba ya ku Silo+ ndipo mzinda uwu udzawonongedwa moti simudzapezeka aliyense wokhalamo’?” Pamenepo anthu onse anali kubwera ndi kuzungulira Yeremiya m’nyumba ya Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena