Yeremiya 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Choncho ine ndidzalanga aneneriwo chifukwa aliyense wa iwo akuba mawu anga kwa mnzake,” akutero Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:30 Nsanja ya Olonda,2/1/1992, tsa. 4
30 “Choncho ine ndidzalanga aneneriwo chifukwa aliyense wa iwo akuba mawu anga kwa mnzake,” akutero Yehova.+