1 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano tumizani uthenga ndipo musonkhanitse Aisiraeli onse kwa ine paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala+ ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”+
19 Tsopano tumizani uthenga ndipo musonkhanitse Aisiraeli onse kwa ine paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala+ ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”+