2 Mafumu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano dziwani kuti mawu onse a Yehova otsutsa nyumba ya Ahabu amene Yehova ananena, adzakwaniritsidwa.+ Yehova wachita zimene ananena kudzera mwa mtumiki wake Eliya.”+
10 Tsopano dziwani kuti mawu onse a Yehova otsutsa nyumba ya Ahabu amene Yehova ananena, adzakwaniritsidwa.+ Yehova wachita zimene ananena kudzera mwa mtumiki wake Eliya.”+