1 Samueli 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzasintha maganizo* chifukwa iye si munthu kuti asinthe maganizo.”*+ Yesaya 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasankha zoti achite,Ndiye ndi ndani amene angazilepheretse?+ Dzanja lake latambasulidwa,Ndi ndani amene angalibweze?+
29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzasintha maganizo* chifukwa iye si munthu kuti asinthe maganizo.”*+
27 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasankha zoti achite,Ndiye ndi ndani amene angazilepheretse?+ Dzanja lake latambasulidwa,Ndi ndani amene angalibweze?+