2 Mafumu 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yehu anakumana ndi abale+ ake a Ahaziya+ mfumu ya Yuda. Atawafunsa kuti, “Ndinu ndani?” iwo anayankha kuti: “Ndife abale ake a Ahaziya. Tikupita kukaona ngati ana a mfumu ndi ana a mfumukazi ali bwino.”
13 Pamenepo Yehu anakumana ndi abale+ ake a Ahaziya+ mfumu ya Yuda. Atawafunsa kuti, “Ndinu ndani?” iwo anayankha kuti: “Ndife abale ake a Ahaziya. Tikupita kukaona ngati ana a mfumu ndi ana a mfumukazi ali bwino.”