2 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehu atangoyamba kulimbana ndi a m’nyumba ya Ahabu,+ anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya,+ omwe anali atumiki a Ahaziya, ndipo anawapha.+
8 Yehu atangoyamba kulimbana ndi a m’nyumba ya Ahabu,+ anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya,+ omwe anali atumiki a Ahaziya, ndipo anawapha.+