2 Mafumu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi yomweyo Yehu anati: “Amuna inu, agwireni amoyo+ anthuwa!” Choncho anawagwiradi amoyo n’kukawaphera pachitsime cha panyumba imene abusa ankameteramo ubweya wa nkhosa. Anawapha onse 42 ndipo palibe amene anamusiya ndi moyo.+
14 Nthawi yomweyo Yehu anati: “Amuna inu, agwireni amoyo+ anthuwa!” Choncho anawagwiradi amoyo n’kukawaphera pachitsime cha panyumba imene abusa ankameteramo ubweya wa nkhosa. Anawapha onse 42 ndipo palibe amene anamusiya ndi moyo.+