Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Choncho mfumu Yehoramu+ inabwerera n’kupita ku Yezereeli+ kuti ikachire zilonda zimene Asiriya anaivulaza ku Rama,* pamene inali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya. Chotero Ahaziya+ mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anapita ku Yezereeli kukaona Yehoramu mwana wa Ahabu chifukwa anali kudwala.

  • 2 Mafumu 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehoramu atamva zimenezi, anati: “Mangirirani mahatchi kugaleta!”+ Chotero anamangiriradi mahatchi kugaleta lake lankhondo. Ndiyeno Yehoramu mfumu ya Isiraeli ndi Ahaziya+ mfumu ya Yuda, ananyamuka aliyense pagaleta lake lankhondo, kupita kukakumana ndi Yehu, ndipo anakumana naye pamunda wa Naboti+ Myezereeli.

  • 2 Mbiri 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako anthu okhala mu Yerusalemu analonga ufumu Ahaziya*+ mwana wake wamng’ono kwambiri, kukhala mfumu m’malo mwake (chifukwa gulu la achifwamba limene linabwera ndi Aluya+ kumsasa linapha ana ake onse akuluakulu).+ Tsopano Ahaziya mwana wa Yehoramu anayamba kulamulira monga mfumu ya Yuda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena