2 Mafumu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake, Yehoramu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 1 Mbiri 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehosafati anabereka Yehoramu,+ Yehoramu anabereka Ahaziya,+ Ahaziya anabereka Yehoasi,+
24 Pomalizira pake, Yehoramu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anayamba kulamulira m’malo mwake.