1 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno panali munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli, umene unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya. 1 Mafumu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, nthawi yomweyo anauza Ahabu kuti: “Nyamukani, katengeni munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, popeza Naboti salinso moyo koma wafa.” 1 Mafumu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+
21 Ndiyeno panali munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli, umene unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.
15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, nthawi yomweyo anauza Ahabu kuti: “Nyamukani, katengeni munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, popeza Naboti salinso moyo koma wafa.”
19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+